Akampani la Syngenta akufuna kuthandizila alimi kuti afutukule ulimi wao ndi kuteteza anthu, nyama ndi chilengedwe.
Timalimbikisa alimi padziko lonse kutsatila Malamulo 5 pogwilitsila nchito mankhwala otetezela ku tizilombo ndi mbewu zopakidwa mankhwala.
Kuti mudziwe zambili onani pa www.pesticidewise.com